Senza, Pt. 2 ft. David Kalilani & Saxess Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2020
Lyrics
Senza mtawo wako
Yeah!
Substance music
The only cross that you carry is a fashionable neck-less
We say we love Jesus, but mayne we live reckless
Akuti ndi artist wa gospelo
Akumagona ndi mahule kumahotelo
Ndi nkhristu?
Amatha kupanga nyimbo
Nanga kupanga ma disciple
it's not simple
Ndi nkhritsu
Amawina ma award!
Nanga kuwina miyoyo ya Awa
IIIIIIIIIHHHHHH
Phukusi la moyo wako osaseweretsa
Ngati tili akhristu chonde tiziziletsa
Tikapusa kuyaka kwathu dziko lizimitsa
Mzinda oyima paphiri ndiovuta kubisa
Iwe senza
Iwe senza
Senza mtanda wako
Unditsate ine anatero Ambuye
Ngati tilibe phewa mtanda tisenza bwanji
Tikwanitsa bwanji mayesero kuwapewa
Kodi ndi nzeru zathu ndizotheka kudziletsa
Ngati mumtima mwathu mulibe Mzimu Woyera
Tiyenda bwanji pamoto beya
Ngati Moto Wonyeketsa satitsogolera
Mavuto akabwera
kuyamba kufila pressure
Ngati Yesu simaziko anthu amasiya kupreza
Mtanda ulibe ubouncer
Ulibe kutchuka ngati radio announcer
Kuwunyamula Kumatheka
Moyo wathu kwa Mulungu kwathunthu tikawuchita surrender
Senza mtawo wako
Kuwunyamula Kumatheka
Moyo wathu kwa Mulungu kwathunthu tikawuchita surrender
Iwe senza
Iwe senza
Senza mtanda wako
Unditsate ine anatero Ambuye