Yehova Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Ngati nyumba samanga Yehova
Oyimangayo amanga chabe
Ngati banja samanga Yehova
Oyimangayo amanga chabe
Ndinveleni Yehova
Ndalila misonzi ndikutopa
Ndinveleni Yehova
Ndalila misonzi ndikutopa ine
Nthawi yozemba inatha
Pano ndabwela
Ndabwela ndi nsembe yopseleza
Ndikupemphela
Mukhululuke machimo anga
Mundilandile
Ndinali ine nkhosa yosochela
Ndazindikila
Ngati nyumba samanga Yehova
Oyimangayo amanga chabe
Ngati banja samanga Yehova
Oyimangayo amanga chabe
Ndinveleni Yehova
Ndalila misonzi ndikutopa
Ndinveleni Yehova
Ndalila misonzi ndikutopa ine
Msambizgi wane
Dada wane
Ndazomelezga vya kukhumba vyinu
Chitani umo mwakhumbira
Pakuti moyo opanda inu ulichabe
Ndazindikila ine
Nzeru zanga
Mphanvu zanga
Mukayikapo dzanja
Zimakhala in abundance
Mbuye palibe chomwe ndingakwanitse ine opanda inu
Palibe
Ngati nyumba samanga Yehova
Oyimangayo amanga chabe
Ngati banja samanga Yehova
Oyimangayo amanga chabe
Ndinveleni Yehova
Ndalila misonzi ndikutopa
Ndinveleni Yehova
Ndalila misonzi ndikutopa ine
Mundinvele ine Yehova
Mundinvele ine Yehova
Mundinvele ine Yehova
Mundinvele ine Yehova