Desire Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Ka nkhope kako kongola
Timawu take tosalala
Khalidwe lako landisangalatsa
Ndi nzimu wako osangalala
Nde tandiuze lako dzina
Chifukwa you're so beautiful and girl
I'm in love with you
Ndakhala kusaka mayiko
Osakupeza darli wanga
Ena imakhala love at first sight
Ine nnadziwa ntakulota
Nde tandiuze lako dzina
Chifukwa you're so beautiful and girl
I'm in love with you
Everytime when I look into your eyes I see fire in there
Timaso takoto thwani my desire ndiwe
Izi sizochita kufunsa ine wanga ndiweyo
Timaso takoto thwani my desire ndiwe
Ndiweyo
Ndiwe
Ndiweyo
Ndiwe
Me and you
Tisapange zokondweletsa Anthu
Ndikati I got you
Mpaka wina nditamuwaza Kung Fu
Sindizasiya kukukonda poti love is not a crime
Be your ride die any day and any time
Limodzi lachepa everyday is valentine
Tsiku ndi limodzi baby I will call you mine
Ndi nkhope yako yongola
Timawu take tosalala
Khalidwe lako landisangalatsa
Ndi nzimu wake osangalala
Nde tandiuze lako dzina
Chifukwa you're so beautiful and girl
I'm in love with you
Everytime when I look into your eyes I see fire in there
Timaso takoto thwani my desire ndiwe
Izi sizochita kufunsa ine wanga ndiweyo
Timaso takoto thwani my desire ndiwe
Ndiweyo
Ndiwe
Ndiweyo
Ndiwe