Mtima Lyrics
- Genre:Soul
- Year of Release:2022
Lyrics
Mtima wanga unasweka ndinkayesa nga wako ndiine ndekha
Zaka zitatu zongobetsa
Kundinamiza nnati ulipo wekha
Ndi chikondi chakhathikhathi nnakupatsa moyo wanga mosabwenza
Pano ntima uli madzi madzi nsozi watsikila komwe unawubwenza
Kuti ukhale mmtima mwanga
Singathe darli wanga
Wandipha mmoyo mwanga
Waupha ntima wanga
Kuti ukhale bwenzi langa
Singathe darli wanga
Wandipha mmoyo mwanga
Bwela ndikuwuze
Za mu mtima, mu mtima
Mu mtima, mu mtima
Muntima mwanga mwadzadza revenge
Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima (muntima)
Muntima, muntima
Muntima
You told me you'd never cheat on me
Always you'll protect my heart hmm
Pano nkakhala mmangoganizila if everything you said was a lie
Unandiuza sunganditonze olo zitavuta Maka
Pano anzanga onse akuwona uli ndi wina
Tell me how did you protect my pride
Kuti ukhale mmoyo mwanga
Singathe darli wanga
Waupha ntima wanga
Waupha ntima wanga
Waupha ntima wanga
Ndikuuze
Ndikuuze
Za mu mtima, mu mtima
Mu mtima, mu mtima
Muntima mwanga mwadzadza revenge
Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima (muntima)
Muntima, muntima
Muntima, muntima
Muntima, muntima
No matter what you say
No matter what you do
Makhalidwe ako andiwopsa
Mtima wangawu sukukhazika
Ungomenya kuti bu bu bu
Bu bu bu bu bu
Ntima wungo gunda gunda gunda
Mmmhhmm hmm hmm hmm hmm
Menya kuti bu bu bu
Bu bu bu bu bu
Ntima wanga umango gunda
Mmmhhmm hmm hmm hmm hmm
They don't know girl
Don't know girl
Oooh ooh ooh yeah