Mwana Lyrics
- Genre:Soul
- Year of Release:2022
Lyrics
Mwana
Oh mwana
Eh mwana
Kale ndili mwana ndisanazitolele
Mabvuto anga anali lamba wa adadi
Ndinkafunitsitsa kukhala pandekha
Poti amama samalola kuyenda ndi usiku
Lero ndakula nyumba ndapeza
Koma chondidabwitsa ndifuna nditakhala mwana
Mabvuto achuluka ntchito kusowa
Koma rent angokweza ambuye ndipangeni mwana
Oh mwana
Eh mwana
Ah mwana
Ndipangeni mwana
Oh mwana
Eh mwana
Ah mwana
Ndipangeni mwana
Kale tili wana ife tinkasonkhelana
Zinthu zikavuta tinkathandizana
Azibale nawo ankatiwona daily poti zinthu zinkayenda
Pano ndakula moyo kulimba
Mmalo mondithandiza amandi gulila mowa
Mabvuto achuluka ntchito kusowa
Koma rent angokweza ambuye mpangeni mwana
Oh mwana
Eh mwana
Ah mwana
Ndipangeni mwana (Ndipangeni)
Oh mwana
Eh mwana
Ah mwana
Ndipangeni mwana (Oh mwana)
Oh mwana
Eh mwana
Ah mwana
Ndipangeni mwana
Oh mwana
Eh mwana
Ah mwana
Ndipangeni mwana