M'malele (Remix) ft. Driemo Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Ooooh yeah
Oh yea
Say now or forever hold your peace
(Oooh yeah)
Kakaland boy
I've never felt like this
Owina ndiwe watsegula bwalo
Nawo mtima wachita chovomera
Ndikonde Iwe
Ona ndavula face mask
Cause I wanna feel some fresh yeah
Poti chikondi chili M'malele
M'malele M'malele
Si ona, ndichite kugwada kapena
Kuti uzindikile opanda Iwe ntha kupenga
Check that, plus ineyo nzakutenge
I like that, ukamasekelela ngenge
Kuyenda ngati nkhondo mwa ka two by two
Palibe osokoneza it's just me and you
Timele mapiko girl I'll fly with you
Poti chikondi ichi chili M'malele
M'malele M'malele M'malele
Chili M'malele
M'malele M'malele
Uyimbe nane, uvine nane
When I saw you I knew I was searching for you
Be my darling
Until we die baby
Ine ndikakondwa you're the reason why
Ukhale nane baby tizikondana
Ucheze nane nkhani tizigawana
Uyende nane ndizikhala ndi khonfi baby
Chibwano chili M'malele
M'malele M'malele
M'malele M'malele M'malele
Chili M'malele
M'malele M'malele
Uyende nane
Ukhale nane
Zikuvuta baby
Ulire nane