Chikondi ft. Kell Kay Lyrics
- Genre:Soul
- Year of Release:2022
Lyrics
Chikondi ooh yeah
Ooh yeaah
Amayi anandifunsa nati
Ababa anandifunsa nati
Junior tanva uli mu chikondi
Tatiuze ukudziwa bwanji
Ndawawuza za ku mtima
Zonse momwe ndinvela
Mami ndapeza wina
Mtimawu wawutenga (Chikondi)
Wanyamula mtima wanga ndikundipatsa wakenso
(Chikondi)
Waona zofooka zanga nane ndaona zakenso (Chikondi)
Walora chikondi changa chisamile pa chakecho eh (Chikondi)
Chikondi, chikondi
Chikondi
Chikondi
Chikondi
Chikondi
You already know
You should never give up on me (Darle wanga)
Ndili nzofooka uzisenze nawo bwanji (Oooh darle wanga)
You should keep on fighting for us
Chikondi sichimagonja
Zolakwika bvomeleza
(Chikondi)
Sichizilala olo pakhale zolakwika (Chikondi)
Sichimagonja olo chiziphinjika ah (Chikondi)
Chikhuzumuka nzake akalakwitsa
Chilibe nkhanza ooh chilibe nkhanza
Chikondi
Chikondi
Chikondi
Chikondi
Wanyamula mtima wanga nawusamalila muchigoba
(Chikondi)
Ndaona chikondi chako pondisamalira ndili lova
(Chikondi)
Suzaponda minga ndikubeleka mpaka muyaya ine
Chikondi
Chikondi yeaah
Chikondi
Chikondi
Chikondi
Chikondi