M'malele Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
I used to pray for a girl like you you're my one and only
I used to pray for times like these you're my testimony
Tikayenda limodzi ndimakhala ndi khonfi baby
Chibwano chili M'malele
M'malele M'malele
Ukhale nane baby tizikondana
Ucheze nane nkhani tizigawana
Uyende nane ndizikhala ndi khonfi baby
Chibwano chili M'malele
M'malele M'malele
M'malele M'malele M'malele x3
Chili M'malele
M'malele M'malele
Uyimbe nane, uvine nane
When I saw you I knew I was searching for you
Be my darling
Until we die baby
Ine ndikakondwa you're the reason why
Ukhale nane baby tizikondana
Ucheze nane nkhani tizigawana
Uyende nane ndizikhala ndi khonfi baby
Chibwano chili M'malele
M'malele M'malele
M'malele M'malele M'malele
Chili M'malele
M'malele M'malele
Uyende nane
Ukhale nane
Zikuvuta baby
Ulire nane