Loading...

Download
  • Genre:Soul
  • Year of Release:2022

Lyrics

Oh woooah wooah wooah


Amayi ndapita ndikafike ku tawuni

Ndanva zambili za atsungwana ku tawuni

Osamba giza nalo khungu lidafila

Amayi ndipiteko ku tawuni


Nkhope yawo ataphoma powder wa mitundu

Sitepe yawo ngati aluyenda pa zithaphwi

Madansi nawo amavina atagwila pansi

Amayi ndipiteko ku tawuni

Amayi ndikafike ku tawuni


Tawuni, tawuni

Tawuni, tawuni

Tawuni woah tawuni

Tawuni, ndikafike ku tawuni


Amayi ndapita ndikafike ku tawuni

Ndithu ndikuopa ati muli umbava mtawuni

Koma ndikapeza ntchito

Mwina nane nkudzakhala bwana

Kumakwela ndege

Uko ku tawuni

Ndikayenda mmisewu yomanga mwakadaulo

Ndikawona nyumba zobelekana mazana

Ndikawone pomwe

Padagona Kamuzu

Amayi ndipiteko ku tawuni

Amayi ndikafike ku tawuni


Tawuni, tawuni

Tawuni, tawuni

Tawuni woah tawuni

Tawuni, ndikafike ku tawuni


Tawuni, tawuni

Tawuni, tawuni

Tawuni woah tawuni

Tawuni, ndikafike ku tawuni


Amayi ine ndafika, ine ndafika

Ku tawuni, ku tawuni

Koma ayi sizoona, ayi sizoona

Zili ku tawuni,ku tawuni

Anthu kugona ndi njala, ku tawuni

Ena olo pogona, ku tawuni

Amangofela dzina, kufela dzina

Lokhala ku tawuni, ku tawuni


Amayi ine ndafika, ine ndafika

Ku tawuni, ku tawuni

Koma ayi sizoona, ayi sizoona

Zili ku tawuni, ku tawuni

Anthu kugona ndi njala, ku tawuni

Ena olo pogona, ku tawuni

Amangofela dzina, kufela dzina

Lokhala ku tawuni, ku tawuni

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234
          -You can log in via below methods-
          Reset password via e-mail
          -or-
          Reset password via e-mail
          Feedback on resetting password
          * It may take a longer time

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status