Mtima ft. Kelvin Sings & Kell Kay Lyrics
- Genre:Soul
- Year of Release:2022
Lyrics
Inde anati kapilire
Koma osati nkanamizire
Kuti chikondi chipitilire
Wandisandutsa wamasiye
You always starting something
Even when i do nothing
Zofooka zanga usandutsa lupanga
Khalidwe lakolo nde landiopsya
Passive aggressive no more
Masiku ake si anowa
Chombo changa ndimanga
Namondwe wamumtima mwanga Ndikamba
Mtima nnapeleka wonse
Nnawelengela ndi zala zonse
I didn't know it'd be one of us
That would tear us apart
So hear from heart
Za mu mtima (mu mtima)
Mu mtima (mu mtima)
Muntima mwanga mwadzadza revenge
Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima
(Muntima)
Muntima (muntima)
Remember how we used to kiss
Every now and then by the beach
You were my
(ride-ride-ride or die)
You were my
(ride-ride-ride or die)
Ndatseguka mmaso ndilibe chilakolako
Unandiseweletsa unandipangaso chipako
Zofooka zanga pa radio ya a Kazako
Chonde pano panga zako
I wish i could pretend
(to love you)
But my heart can't recommend
Kungofuna revenge
(aaaah)
Oh yeah yeah yeah
(aaaaah)
Ziwalo zanga sizikufunanso
Mayi wanga sakufunaso
Anzanganso sakufunaso
Maloto angawa
Sakulotanso
Za mu mtima (mu mtima)
Mu mtima (mu mtima)
Muntima mwanga mwadzadza revenge
Ndikufuna nditakhala ndi iwe koma muli mdima
(Muntima)
Muntima (muntima)
(Muntima)
No matter what you say
No matter what you do
Makhalidwe ako andiwopsa
Mtima wangawu sukukhazikika
Ungomenya kuti bu bu bu
Bu bu bu bu bu
Ntima wungo gunda gunda gunda
Mmmhhmm hmm hmm hmm hmm
Menya kuti bu bu bu
Bu bu bu bu bu
Ntima wanga umango gunda
Mmmhhmm hmm hmm hmm hmm