Give up on me Lyrics
- Genre:Soul
- Year of Release:2022
Lyrics
You should give up on me
Give up on me
Sindizakukondaso
Sindizakukondaso
You should give up on me
Give up on me yeah yeah yeah
Hhmmm
We had a lot of good dreams
We had a lot of good things yeah
Tinalonjezana zambiri
I told you sindizakusiya iwe
Koma tinamanga pa nchenga
Nyumbayi pano nkani yatigwela
And we can never fix it
Mmh move on
And you should give up on me
Give up on me
Sindizakukondanso
Sindizakukondanso
You should give up on me
Give up on me yeah yeah
Sindizakukondanso
Sindizakukondanso
I remember the first time iwe utathetsa zinali zonvesa chisoni
After miyezi khumi tinajailana kuthetsa sikunali nkhani
Lero wapita mawa wabwela
Lero ndapita mawa ndabwela
The only reason we were together
Is we got too used to each other
We had a lot of good dreams
We had a lot of good things yeah
Tinalonjezana zambiri
I told you sindizakusiya iwe
Koma tinamanga pa nchenga
Nyumbayi pano nkani yatigwela
And we can never fix it
Move on, move on
And you should give up on me
Give up on me
Sindizakukondanso
Sindizakukondanso
You should give up on me
Give up on me yeah yeah
Sindizakukondanso
Sindizakukondanso
Ndinakuuza ndinkanena
Unkaletsa kumandigenda
Koma maboza amapha tikulenga
Ndinanena
Ndinakuuza ndinkanena
Unkaletsa kumandigenda
Osakamba bodza ngati ulibe chonena
Ndinkanena
Ndatopa ndikumenyana
Panopa ndingofuna bata
Ndatopa ndiku kangana ndatopa
I know zonse nnakuuza
Nnati sindizakusiya
I thought mtima unasankha pano wakana
And you should give up on me
Give up on me
Sindizakukondanso
Sindizakukondanso
You should give up on me
Give up on me yeah yeah
Sindizakukondanso
Sindizakukondanso
You should give up on me
Give up on me
Sindizakukondaso
Sindizakukondaso
You should give up on me yeah yeah