Kusangalala ft. LeuMas Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2023
Lyrics
Kusangalala ft. LeuMas - Zeze Kingston
...
usangalala Lyrics
Eyoh tiyeni
Tiyeni tiyeni tiyeni iiishi
Unanana unanana mmmh
Unanana unanana mmmh
Pomwe ena akulira ena akuseka mmmmh
Mmh pomwe ena akulira ena akusekelera
Koma masiku ako osekelera sangakhale onse dziwa
Ndati masiku ako ovutika sangakhale onse dziwa
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Olo ndi dziliraaah! Ndilira mpaka liti?
Ndi dzidandaulaaah! Ndi dandaula mpaka liti?
Olo ndi dziliraaah! Ndilira mpaka liti? (Ndilira mpaka liti?)
Ndi dzidandaulaaah! Ndi dandaula mpaka liti?
(ndi dandaula mpaka liti?)
Poti mavuto samatha (mavuto samatha)
Poti mavuto samatha (mavuto samatha)
Poti mavuto samatha (mavuto samatha)
Poti mavuto samatha (mavuto samatha)
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri koma
Ine ndasakha kusangalala