Alamu Anu ft. Nyasapiano Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2023
Lyrics
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu

Ayiwala zonse, tinakambilana zija
Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza
Koma kungochoka osanena, unangondiyuza

Koma kungochoka osanena, unangondiyuza eish!
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu
Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu
Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu
Ayiwala zonse, tinakambilana zija
Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Apeza wanyowani, avuta mma status
Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Ngati ndakutopetsa vuto ndi chani, osangondiuza