Kusangalala ft. LeuMas Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2023
Lyrics
Pomwe ena akulila ena akusekelela
Pomwe ena akulila ena akusekela
Koma masiku ako osekelela
Sangakhale onse dziwa
Ndati masiku ako ovutika
Sangakhale onse dziwa
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Olo ndizilila ndilila mpaka liti
Ndizidandaula ndidandaula mpaka liti
Olo ndizilila ndilila mpaka liti
Ndilila mpaka liti
Olo ndizidandaula mpaka liti
Poti mavuto samatha
Mavuto samatha
Mavuto samatha
Mavuto samatha
Mavuto samatha
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwisa ndizambili
Koma ine ndasankha kusangalala
Kusangalala
Kusangalala
Kusangalala
Kusangalala