![Mphaka ft. LeuMas, Achina Gattah Ase, DJ Drew & Richard Billy](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/09/09/e7d64b2d57c044f7bc31ff984fc3ae84H3000W3000_464_464.jpg)
Mphaka ft. LeuMas, Achina Gattah Ase, DJ Drew & Richard Billy Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2023
Lyrics
Eyo Tiyeni
Tiyeni Tiyeni Tiyeni
Wadzuka bwanji neba
Ndiwe o obeba
Ufunika mwamuna woti zake zikuyenda
Kamwamuna kako kakhoza kuyenda
Chabwino katsale chifukwa kakhodza kugenda
Koma akangosuntha
Ndizibwela kwanu kuzafuntha
Ine ndimfana wanjalatu
Ndizibwela kwanu kuzakhuta
Christina
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Ndati
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Eyo Tiyeni Tiyeni Tiyeni
Ndapeza mu tea athilamo milo
Athilamo milo
Bread mpakana ma pisi folo eeh
Mpakana ma pisi folo
Mowa wanga andimwela
Ndapeza mowa wanga andimwela
Ndatsegula mu fridge mwanga
Ndichi confidence nyama yonse andidyela
Ndapeza mu tea athilamo milo
Athilamo milo
Bread mpakana ma pisi folo eish
Mpakana ma pisi folo
Mowa wanga andimwela
Ndapeza mowa wanga andimwela
Ndatsegula mu fridge mwanga
Ndichi confidence nyama yonse andidyela
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Mphaka wachoka
Makhoswe atase
Wadzuka bwanji neba
Ndiwe o obeba
Ufunika mwamuna woti zake zikuyenda
Kamwamuna kako kakhoza Kuyenda
Chabwino Katsale chifukwa Kakhodza Kugenda
Koma akangosuntha
Ndizibwela kwanu kuzafuntha
Ine ndimfana wanjalatu
Ndizibwela kwanu kuzakhuta
Christina
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Ndati
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Mphaka wachoka
Makhoswe Atase
Eyo Tiyeni Tiyeni Tiyeni
Ndapeza mu tea athilamo milo
Athilamo milo
Bread mpakana ma pisi folo eish
Mpakana ma pisi folo
Mowa wanga andimwela
Ndapeza mowa wanga andimwela
Ndatsegula mu fridge mwanga
Ndichi confidence nyama yonse andidyela
Ndapeza mu tea athilamo milo
Athilamo milo
Bread mpakana ma pisi folo eish
Mpakana ma pisi folo
Mowa wanga andimwela
Ndapeza mowa wanga andimwela
Ndatsegula mu fridge mwanga
Ndichi confidence nyama yonse andidyela