Go Go Go ft. Leumas & Afana Ceez Aidfest & Kineo Madness Imnotsteelo Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2024
Lyrics
Go Go Go ft. Leumas & Afana Ceez Aidfest & Kineo Madness Imnotsteelo - Zeze Kingston
...
Gogogogogo Ali pakhomo
go go go Ali pakhomo ×4
ayo tiyeni tiyeni tiyeni tiyeni
6am Ali pakhomo
ATI akufuna m'memo
eish olo chibuku pot kudya kuli mmomwemo
ati zeze bwanji mowa
kuno .........samasowa
eish mumowa munasowa
segula ndingolowa
at eish zeze bwanji mowa
kuno .........samasowa
dzulo ku mowa kunabowa
segula ndingolowa
kma abale uyuyu uyu ndnampeza kut uyuyu uyu
eish uyuyu uyuyu uyu
andithesera banja uyuyu uyu
akati gogogogogo Ali pakhomo
Ali pakhomo eish
et go go go Ali pakhomo
Ali pakhomo
Inu et gogogogogo Ali pakhomo
Ali pakhomo
ndafika kale
eish go go go Ali pakhomo
Ali pakhomo
6 am Ali pakhomo
gogogogogo Ali pakhomo
Ali pakhomo
go go go Ali pakhomo
Ali pakhomo
gogogogogo Ali pakhomo
Ali pakhomo
go go go Ali pakhomo
ine nditere Ali pakhomo
eish go go go Ali pakhomo
Ali pakhomo
wafka kale Ali pakhomo
ey ey ey ey ey ey ey
ayo tiyeni tiyeni tiyeni tiyeni
go go kagone unaliko
watikwana pano
ukufuna nsima ngat unasiya ya ndiwo
akati go go go
kagone unaliko
watikwana pano
ukufuna nsima ngat unasiya ya ndiwo
Neighbor Ali pakhomo
madam ansekera khomo
akuti unaliko
ukagone komweko
Neighbor Ali pakhomo
madam ansekera khomo
akuti unaliko
ukagone komweko