Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu - Gwamba
...
(VERSE 1)
Yohh ndika khala ndekha Ndazimisa Phone ndangoshala Penapake Ndili Lonely Mutu Mwangamu Mumayenda Zambiri, Reflection Yeni Yeni yomwe ine ndili koma ndika khala Fans Ikowona Ndimafuna Ndinama ngat Ndine Obona Komano Kweni Kweni Manamiza Ndan, Beef Thupi Ndi Zimu wanga udani Ndika khala Mu Church Ndimamenya MA Lilime Komano Mzimu Oyela Sumakhala Ulindine Pakamwapa Ku Thoka Koma Mutu muli Zina Olungama PA Maso Koma Nkatimu ndi Sinner
(HOOK)
Ngakhale Mchipinda Mopanda Amene akuona eee ulengeni Mtima wangawu eeeee Ukhale Ngati Inuuuuuuuuuuuuuu In Everything I doooooooooooooooo Ukhale ngat (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba) In Everything I Do (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba)
(VERSE 2)
Nde In Everything I Do Mundithandize kukhala Odekha Poti Ndinabadwa ndizapita Ndekha(and it's True) ndizapazikozi Ndimakopeka, Tsoka Mukafuna Kunditenga Osakonzeka Pena ndima Seka Muntima Muli Misonzi , Anthu amangoona Nkamasekelela Chonchi, Koma Zamu Ntima Mwanga Amadziwa ndi Modzi Nde Pakati pa Dziko Ndi Yesu ndisankhe Modzi, Pena Ndimaseka Muntima Muli Misonzi Anthu Amangoona Nkamasekelela Chonchi Koma Zamuntima Mwanga amadziwa ndi modzi, Pakati pa dziko Ndi Yesu ndisankhe Modzi...
see lyrics >>Similar Songs
More from Gwamba
Listen to Gwamba Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu MP3 song. Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song from album True Independence is released in 2022. The duration of song is 00:03:20. The song is sung by Gwamba.
Related Tags: Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu, Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song, Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu MP3 song, Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu MP3, download Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song, Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song, True Independence Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song, Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song by Gwamba, Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu song download, download Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu MP3 song
Comments (23)
New Comments(23)
Ernest 2yybd
Powerful
Allegal Georman
nyimbo iyiyi on repeat today eish
Mundy Nando Kadelera
nice track sir
hopehb34l
GOAT
DAVID ibw5n
song of the month
Mphatso Phiriud3me
kelvin sings umatha
JOSHUA KADULIR
Fire [0x1f63f][0x1f63f]
Wizzie Kambuzi
[0x1f63f][0x1f63f]
Chris p9h09
nice
Nelsong9h8v
[0x1f63f][0x1f63f][0x1f63f][0x1f63f]
Amuna bato
Kelvin Sings on it again Love the melody in it
gwamba umatha ase