6-2-6 ft. Temwah, XDuppy & Quayr.Musiq Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2022
Lyrics
Aaah aaah aaaah aaah
Ndamuona mkazi wako wangokhala wangokhala
Ndamuona mkazi wako wangokhala wangokhala
Kumuyitana sakukana sakukana
Ndamuyitana sakukana sakukana
Ndati umwa chani, umwa chani, Hennessy olo cider
Ati ayi, shot ya Tequila
Umwa chani, umwa chani Hennessy olo cider
Ati ayi, Shot ya tequila
Ndiye tilipano tilipano, party 6 to 6
Barman mowa ulikuti?
Tilipano tilipano, party 6 to 6
Barman, mowa ulikuti
Tilipano tilipano, party 6 to 6
Barman mowa ulikuti
Tilipano tilipano, party 6 to 6
Barman, mowa ulikuti
Ndilipano, ndilipano, party 6 to 6 ye ey ey ey
Ndilipano, ndilipano, party 6 to 6 yeee eeeh
Ndilipano, ndilipano, party 6 to 6 ye ey ey ey
Ndilipano, ndilipano, party 6 to 6 yeee eeeh
Wandifunsa umwa chani Dom Perignon
Wandifunsa umwa chani Dom Perignon
Wandifunsa umwa chani Dom Perignon
Wandifunsa umwa chani Dom Perignon
Iyeee yeeeeee
Ayi ayi ayi ayi eish!
Ndamuona mkazi wako wangokhala
Ndamuona mkazi wako wangokhala
Kumuyitana sakukana
Ine ndamuyitana sakukana
Ndati umwa chani, umwa chani, Hennessy olo cider
Ati ayi, shot ya Tequila
Umwa chani, umwa chani Hennessy olo cider
Ati ayi, Shot ya tequila
Ndiye tilipano tilipano, party 6 to 6
Barman mowa ulikuti
Tilipano tilipano, party 6 to 6 ye yeeey
Ndilipano ndilipano, party 6 to 6 yeeee eeey
Ndilipano ndilipano, party 6 to 6 yeeee eeey
Ndilipano ndilipano party 6 to 6
Barman mowa ulikuti