Maluzi (Remake) ft. LeuMas & Amfumu Collins Bandawe Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2023
Lyrics
Maluzi (Remake) ft. LeuMas & Amfumu Collins Bandawe - Zeze Kingston
...
ndizutseni zutseni nsagoneleze
kuzuka mmawa ulendo waku msika geni kugulutsa poti ndalama zavuta
kuzuka mmawa ulendo waku ntchito kuthamangitsa failo poti ndalama zavuta
aaaah mmh ndayendayenda kufunafuna ntchito ndalephela
ndazungurila ku Blantyre ntchito sindinayipeze
ndatchekela maluzi ndalephela ine eeeh
ndayendayenda ndiliphuwanoko ku Lilongwe
ndayesayesa kuitanila ma mini bus ine
ndatchekela maluzi ndalephela ine eeeh
aaah ine ine ndatchekela maluzi ndalephela
ndangosanduka waminyama
ndatchekela maluzi ndalephela
ndangosanduka olira
tchekela maluzi ndalephela aaah ine ine ndatchekela maluzi ndalephela
ndangosanduka osauka ndatchekela maluzi ndalephela
ndangosanduka olira tchekela maluzi ndalephela
ine . ine . maluzi . maluzi
ayi tiyeni tiyeni tiyeni eiish
munthu wandalama kuitana okukonda ambiri
pano vuto likubwera kumasowa oti aku ndandize
pakhomo Pako mitu kuombana ngati pa guwa
miyanja opata dziko lapansi likulamila Kwa amphawi abale
okhala osauka palibe chikuti komela
munthu waumphawi kumakhala ngati choncho iiih
mukagula mutuusule wankhonya nkhonya mavuto sakuchoka