Chule ft. Afana Ceez, Tuno Mw, Leumas & Vj Ice Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2023
Lyrics
Chule ft. Afana Ceez, Tuno Mw, Leumas & Vj Ice - Zeze Kingston
...
Wakutuma ndan ungandiuze chani 2x,munthu opanda plan ochulukisa nkhan ungandiwuze chani chule chule iwe kt bwatasa wakutuma ndan kt ubekeshule bwatasa mwana wachipongwe ,ndakula movutika man mulibe nkhan mukachulukisa nkhan ife tingokuwekan 2x ....................wachibanda ndan zakulemban akufuna plan ndan tisachuluse nkhan