Lemba Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Kusokoneza ubongo
Basi choncho
Kunong'oneza bondo
Basi choncho
Kusokoneza ubongo
Basi choncho
Kunong'oneza
Zambiri ndikonda nzondisocheretsa aaah
Ndi zoipa koma ndi zondikondweretsa aah
To make things worse zindivuta kupewa aah
Ndi zomwe zikuthandiza moyo wu kufewa
Ndazizidwa ndiholdeni (Holden)
Musalole ndibalalike
Ndifuna inu ndine tibonde (Tibonde)
Nkhope yanu isabisike
Ndachita zambiri against your laws
Please forgive me first of all
And I know for sure zonse munandipatsa
Aaah
Malemba
Ndiwerenge malemba
Kuti pena ndikasochera ndidzikumbuka malemba
Malemba
Ndiwerenge malemba
Kuti pena ndikabalalika ndidzikumbuka malemba
Kunjaku ndiri bho di (bold)
Kunjaku kuli golide
Ndungomva odi, moni (moni)
Moyo wanga ndi quality
Ena kufeela
Ena kuchita kufeela
Koma ndine sinner
Ndichita zina
Zomwe sadziwa
Koma ndisachite izizi over
Mukwanitse izi ku Solva ah
Pena ndipemphera ndikununkhira Bibida
A believer koma ndigona ndi chida
Malemba
Ndiwerenge malemba
Kuti pena ndikasochera ndidzikumbuka malemba
Malemba
Ndiwerenge malemba
Kuti pena ndikabalalika ndidzikumbuka malemba
Basi choncho
Kusokoneza ubongo
Basi choncho
Kunong'oneza bondo