Mtunda Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Mtunda - PiksyMw
...
ARTIST: Piksy
TITLE: Mtunda
u can never love someone else
if don't love yourself (self love)
ka mtima kangaka kukonda kunjoyaka
kukonda kubolaka
kamakonda mowaka
ka mtima kangaka kukonda kujedaka
kukonda kusekaka
koma sikachedwa kuswekaka
komano ka mtimaka
ndikokula mtimaka
ndipeze time
ndikhale nako pansi
ndizilangize
ndizikhanzike pansi
ndizikumbutse( mtundawu ndiwa ndekha)2x
yooh!!!!
ka mtima kanga nkosayamika
kusiya kalinazo kafuna zina
Kali ndi VW kafuna BEAMER
ati kutsidya the grass greener
always searching for doze
always looking for more
mu mtima zinkhawa zilitho
mkumazinamiza kalibho
komano ka mtimaka
ndikokula mtimaka
ndipeze time
ndikhale nako pansi
ndizilangize
ndizikhanzike pansi
ndizikumbutse( mtundawu ndiwa ndekha)2x
koma ndikachondelera
kachepetse kudyelera
kadzikonda kupephera
ndikhala nane pansi (2x)
BACK TO CHORUS ^