Anana Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Anana - PiksyMw
...
...
Yoh Foxy, Chi Piksy Chi Mfana Chodziwika ndi Boma
....
Zinayamba mwachibwana
Timashopa Gymkana
Ife tilibe chikwama
Enawa amkatikana
Kukwiya tikasanja
Kumaseka tikanjanja
Osalakwa kutilanga
Kutiyang'anila under
Kufeela ngat mlendo
Kukhala ngati Zoba, opanda Frenzo
Koma ndi chi Hope kugwira ntchito
Anawa apanda mavuto onse history
. .
Ndeno zikatele itsanana
Tele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Tele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Pano tili ku mtunda tikumatha kumajambula video kunja
Zomwe sitinkadyazo tikudya
Sitiyenda pansi nde tili ndi nyumba
Kale ankadutsa kupita osapatsa moni
Kuimba osayankha phone
Podutsa maninja kuika stones
Pena ngati ungopita Joni
Lero holiday, Namibia
Pop that champagne again waziziwa
Sikuti funa kunena kut wandilira
Uwu ndi Umboni wanga mphwanga ndinashupika ndeno
Zikatele itsanana
Tele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Tele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Uuuh thank God for life
Thank God for everything
Coz paliponse pamene you are
Aliponso wina wake amapafuna
Uuh thank God for life
Thank God for everything
Coz paliponse pamene you are aliposo wina wake amapafuna
Tsono
Zikatele itsanana
Tele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Zikatele itsanana
Tele it's anana
Zikatele it's anana
Zikatele it's anana
Zikatele ( it's anana)
Tele it's ananana
Zikatele it's anana