Not Today Devil Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Saturday wangodzuka bwino olo kukhosomola
Once again moyo wabwino ukulondolola
Mphasha ya chabe ya mu suitcase wangoyisosola
Nyimbo zabwino ziri mmutu mwako zikulongolola
Then comes the devil, misampha watchera
Akutsitse level, koma osamvera
Nde ukhale stable, lero osamgwera
And God is able, Khala okondwera
saying
Not today devil
Not today
Not today no no
Not today
Not today devil
Not today
Not today no no
Not today
Not today
Apapa ndakonzeka

hoooooooo
Saturday wangodzuka bwino olo kukhosomola
Saturday wangodzuka bwino olo kukhosomola
Saturday wangodzuka bwino olo kukhosomola
Saturday wangodzuka bwino olo kukhosomola