Nzanga Lyrics
- Genre:R&B
- Year of Release:2022
Lyrics
Nzanga - PiksyMw
...
........
........
Mzanga uli bwanji
Zikuyenda bwanji,
How's your family
Business ikuyenda bwanji,
Poti zikoli ndiye lavuta kwambri
Ona daily tikuluza fans
Kaya chaka chino zitithera bwanji
Everyday kugwada pansi
Mulungu akhululukile dziko lapansi
Please hold on my friend
Stay strong, its gonna be a bumpy road
I have hope my friend, we gonna be al-right
Koma pompano tikumana
Tiyese kuzisamala
Posachedwa kuwala
Mwina tingozisamala
Osaopa mzanga
Poti kukondwa ndi mawa
Pompano kuwa-la
We gonna dream to these days
I miss those trips to the lake
Zima boat-ride uku tikusekelera
Achina dj clips on the deck
Tikuvina ndi ma cup tikumwemwelera
Koma wapita-pita-pita-pita
Tingosamalira mwina tizawina
Ayiya-yiya-yiya-yiyaa
Tingosamalira mwina tizawina
Koma pompano tikumana
Mwina tingozisamala
Posachedwa kuwala
Tiyese kuzisamala
Osaopa mzanga
Poti kukondwa ndi mawa
Pompano kuwa-la
We gonna dream to these days
Ayiya-yiya-yiya-yiyaa
Ayiya-yiya-yiya-yiyaa
Ayiya-yiya-yiya-yiyaa
Ayiya-yiya-yiya-yiyaa
Yes i miss church
I miss family
I miss being in the gym
I miss hiking
I miss those shows
I miss y'all
pliz stay safe my friend