Sochera ft. Ritaa Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Ndikaseka ndiwe
Ndikakondwa
Wina sindifuna umakwanirita moyo wanga
Muntima mwanga ineyo
Ulimo wekha iweyo
Ngati uli nyimbo iweyo
Ndimvera yomwe yomweyo
oooh oooh
Poti ndiwe wekha ndifu
Ngati ndi chakudya I'm full
Ndiwe full stop
Ndiwe full stop
Baby
Life is easy
Ulipo pambalipa
Iwe ndi ine zolembedwa kumwamba
Kodi ndingatani ine
Popanda nthiti yane
Darling
Darling
Popanda iwe ndisochera
Ndimakufeela kwambiri
Tsiku ligogoma tikakhala awiri
Iyi ndi love ya mu filimu
Chirichonse chomwe ukufuna I'm willing
Babe this love is giving
Babe be sure I'm not leaving
Tikuyaka moto ifeyo
Tizisiye level yomweyo
Oooh oooh
Poti ndiwe wekha ndifu
Love youluka pruu pruu
Ndiwe full stop
Ndiwe full stop baby
Life is easy
Ulipo pambalipa
Iwe ndi ine zolembedwa kumwamba
Kodi ndingatani ine
Popanda nthiti yane
Darling
Darling
Popanda iwe ndisochera
Poti mwa iwe ndikondwera
Si momwe moyo ukomera
Sindingathe kukuchokera
Popanda iweyo ndisochera
Poti mwa iwe ndikondwera
Si momwe moyo ukomera
Sindingathe kukuchokera
Popanda iweyo ndisochera
Life is easy
Ulipo pambalipa
Iwe ndi ine zolembedwa kumwamba
Kodi ndingatani ine
Popanda nthiti yane
Darling
Darling
Popanda iwe ndisochera