Nzanga Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Nzanga - PiksyMw
...
Mnzanga uli bwanji Zikuyenda bwanji How is your family Business ikuyenda bwanji Poti dzikoli nde lavuta kwambiri Nkona daily tikuloza fanzi Kaya chaka chino zitithera bwanji Everyday kugwada pansi Mulungu akhululukire dziko lapansi Please hold on my friend stay strong Its gonna be a bumpy road I have hope my friend we gonna be alright Koma pompano tikumana Tiyese kudzisamala Posachedwa kuwala mwina tingodzisamala Osaopa mnzanga poti kukondwa ndi mawa Pompano kuwala we gonna drink in these days I miss those trips to the lake Zima boat ride uku tikusekelera Achina DJ Clips on the deck Tikuvina nd ma cup tikumwemwelera Koma wapita-pita-pita-pita-pita Tingosamalira mwina tidzawina Aai-yah-iyah-iyah-iyah Tingosamalira mwina tidzawina Koma pompano tikumana Mwina tingodzisamala Pasachedwa kuwala tiyese kudzisamala Osaopa mnzanga poti kukondwa ndi mawa Pompano kuwala we gonna drink in these days Aai-yah-iyah-iyah-iyah Aai-yah-iyah-iyah-iyah Aai-yah-iyah-iyah-iyah Aai-yah-iyah-iyah-iyah Yes I miss church, I miss family I miss being in the gym I miss hiking I miss those shows I miss you all please stay safe my friends