Chonchobe Lyrics
- Genre:Acoustic
- Year of Release:2020
Lyrics
Chonchobe - PiksyMw
...
foxy i see you
piksy aaye ena adzatsala
mboba osaphwekesa
game pa mwamba osadekhetsa
fans yavaya utsala wekha
ukapusa sudzawapeza
siukudabwa kunfila neighbor
ndeno madolo aku pretender
timawadziwa nde tingoseka
kutinamiza they doing better
mukunva bwanji nthupi
chonchobe
bwanji mwavala juzi
chonchobe
ma post timawaona dona oh sorry
timadziwa kuti mukunama koma
chonchobe
akuchita kuvala mbina
aonekeko bo pa picture
kukumana naye ndi munthu wina
koma iyi ndi nkhani ya tsiku lina
social media mboba sinama
kukhalira kunamiza atsikana(umakwana)
koma aaye ena adzatsala
nokha mupeze ma ansala
mukunva bwanji nthupi
bwanji mwavala juzi
chonchobe
ma post timawaona koma oh sorry
timadziwa kuti mukunama
koma chonchobe
mukunva bwanji nthupi
chonchobe
bwanji mwavala juzi
chonchobe
ma post timawaona dona oh sorry
timadziwa kuti mukunama
koma chonchobe
kupanga tweet ku chiller ndima dada
ku mount soche muli pa zode
kutenga selfie ma chills ndi ma girls
4 seasons muli pa mbowe
mukunva bwanji nthupi
chonchobe
aaye ena adzatsala,mboba osaphweketsa(ndinu bwana)
nokha mupeze ma ansala
mukunva bwanji nthupi
chonchobe
bwanji mwavala juzi chonchobe
ma post timawaona koma oh sorry
timadziwa kuti mukunama koma
chonchobe
mukunva bwanji nthupi chonchobe
bwanji mwavala juzi chonchobe
ma post timawaona dona oh sorry
timadziwa kuti mukunama
koma chonchobe
mukunva bwanji nthupi
chonchobe
bwanji mwavala juzi chonchobe
ma post timawaona koma oh sorry
timadziwa kuti mukunama
koma chonchobe
mukunva bwanji nthupi chonchobe
bwanji mwavala juzi chonchobe
ma post timawaona dona oh sorry
timadziwa kuti mukunama
koma chonchobe
aaye ena adzatsala