
If I Had a Choice Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
If I Had a Choice - Gwamba
...
Ndinalandila phone kuchoka kwa nafe lero ku stuu
Kunabwera mfana winawake
Ama spitta bhooo
Komanso ndiwa humble
Ndika mixer nyimbo imodzi nditumiza sample
Komanso ndiwa fast ka talent Ali nako
One hour anamenya ma verse angapo
Ndi mfana wa bhoooooo amaziwa zochita mutaimba limodzi nyimbo limodzi ikhoza ku heater
Anati abweranso mmawa akapeza ya bus
Amakhala ku ghetto mbali zakuma chance
Akabwera ndikuuza nawe uchizape
Umupemphe Bensam kuti azakutrape
Koma mutamenya ndi crazy anthu atatu
Ndikuuza ase ithaa kukhala nyimbo ya sharp
Tiyeni tizingophusha nafe tizatchuka tsiku lina makomo onsewa azaseguka
(Chorus )
If I had a choice bwezi tonsefe titakhala mpaka kale
I know you had a choice koma Yehova zonsee amaziwa kale (×2)
Takumana ku Stud kodi tipange bwanji ? Tipange remix hit song ya D banj
Wina apo kulemba ma verse mwansanga nsanga kupanga connect kenako kukhala mzangaaa
Masten anga anasanduka ake pa den kudziwa Duncan Ali nd Mzake
Ngini ndyaa simple after tonse nd akumpoto
Koma tikati tishupitse nd mayi kotoooo
Wina zimuvuta nde kulinso Bamthiiii
Kaya sinduziwa tili ndi ma hit angati
Kutchuka nkonsayamba kuyamba kumenya ma concept
Mbiri yathu ku Malawi kufika konsekonse
Kuyambana ndikosayamba umadziwa ma Eagle
Koma ndimakondwa ukamavaya mmaiko
Mtumbika osamba akukaimba ku USA
Koma unali mfana olusa
(Chorus)
If I had a choice bwezi tonsefe titakhala mpaka kale
I know you had a choice koma Yehova zonsee amaziwa kale (×2)
Ndinalandila phone mzako uja wapita
Ine kugwira mutu wanga osatsimikiza
Kuyesa ndikulota kuti mwina ndidzuka
Koma kudabwa kuti tsiku lonse likudusa
Mafunso anga pano akusowa Yankho
Sindinkadziwa kt ndizalemba nyimbo yako
Komano Amati tisamakhweshe namalenga
Nde chilichonse amalengacho timangotenga
Kaya Ngozi kaya matenda
Anali mzangaaa dzulo ndamuona akuyenda
Komano imfa yako yandiphunzitsa lesson
Kuti sithawika ndipo mmawa ndiinenso
Pamalilo pako boma kutenga advantage
Chikondi choti uli moyo sanakupase eti
Mtumbuka osamba mpaka kuzazitsa Civo
Sunali mfana wa simple