Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Ngati Inu ft. Kelvin Sings & Lulu - Gwamba
...
(VERSE 1)
Yohh ndika khala ndekha Ndazimisa Phone ndangoshala Penapake Ndili Lonely Mutu Mwangamu Mumayenda Zambiri, Reflection Yeni Yeni yomwe ine ndili koma ndika khala Fans Ikowona Ndimafuna Ndinama ngat Ndine Obona Komano Kweni Kweni Manamiza Ndan, Beef Thupi Ndi Zimu wanga udani Ndika khala Mu Church Ndimamenya MA Lilime Komano Mzimu Oyela Sumakhala Ulindine Pakamwapa Ku Thoka Koma Mutu muli Zina Olungama PA Maso Koma Nkatimu ndi Sinner
(HOOK)
Ngakhale Mchipinda Mopanda Amene akuona eee ulengeni Mtima wangawu eeeee Ukhale Ngati Inuuuuuuuuuuuuuu In Everything I doooooooooooooooo Ukhale ngat (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba) In Everything I Do (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba)
(VERSE 2)
Nde In Everything I Do Mundithandize kukhala Odekha Poti Ndinabadwa ndizapita Ndekha(and it's True) ndizapazikozi Ndimakopeka, Tsoka Mukafuna Kunditenga Osakonzeka Pena ndima Seka Muntima Muli Misonzi , Anthu amangoona Nkamasekelela Chonchi, Koma Zamu Ntima Mwanga Amadziwa ndi Modzi Nde Pakati pa Dziko Ndi Yesu ndisankhe Modzi, Pena Ndimaseka Muntima Muli Misonzi Anthu Amangoona Nkamasekelela Chonchi Koma Zamuntima Mwanga amadziwa ndi modzi, Pakati pa dziko Ndi Yesu ndisankhe Modzi...
(HOOK)
Ngakhale Mchipinda Mopanda Amene akuona eee ulengeni Mtima wangawu eeeee Ukhale Ngati Inuuuuuuuuuuuuuu In Everything I doooooooooooooooo Ukhale ngat (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba) in Every thing I do (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba)
(VERSE 3)
Pakamwa panga Mupakonze Mtima wangawu Muwupinde Nzeru Zangazi Muzipindee, Zochita Zanga Ziyamike Inuuuu, Munandilenga Bwino Bwino Kufuntha Kwanga Kwaonjeza Ndizipemphelela Chakudya Olo Anzanga Asakuwona, Munandilenga Kwandekha Munandipasa Zandekha Ouuuuuuuuuuu. Ouuuuuuuuuu
(HOOK)
Ngakhale Mchipinda Mopanda Amene akuona eee ulengeni Mtima wangawu eeeee Ukhale Ngati Inuuuuuuuuuuuuuu In Everything I doooooooooooooooo Ukhale ngat (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba) in Every thing I do (Ufanane Nanu baba, Ufanane baba)