
Mumapemphero ft. Namadingo, Temwah & Lawi Lyrics
- Genre:Pop
- Year of Release:2024
Lyrics
Mumapemphero ft. Namadingo, Temwah & Lawi - Gwamba
...
nahhh....namadingo mmhhh
gwamba ...mmhhh
dzanja langalakumanja ndalikwezamwamba ndi malakhula zonsaveka khutu lamunthu
penandi guduka ineeh angati munthu wam'bisala eeeh nzimu wanga ukamvanjala... ine ndimapemphera, chauta amamvetsera ndipo samalephera