Better ft. EmmQ & Tammy Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2016
Lyrics
Better ft. EmmQ & Tammy - Gwamba
...
udziwe Mbuye ali nafe
ngati Mbuyeyo ali nafe
zingodziwa, zidzakhala better
zidzakhala better
Ambuye atisamala
pa mavuto pa mtendele atithangata
uzingodziwa zidzakhala better
zidzakhala better
ndikudziwa nthawi zina umadzifunsa
ukaona zipsinjo zomwe ukudutsa
mbuye kulibe aliko?
akundimva aliko?
mafunso omwe iwe umadzifunsa
nthawi Zina mpaka kuganiza zotsutsa
ndikudziwa nthawi zina umadabwa
umapemphera koma ukugonabe osadya
akuchotsa ntchito zinthu zoti sunapange
pena umadzifunsa Mulungu State,
ndinapanga chani kuti dziko lindilange?
Kaya ndiwe bwana Kaya ndiwe lova
ngati uli moyo uzingoyamika Yehova
Mbuye amakukonda uzikhala pa easy
sangalole ukhale ndi vuto sungakwanitse
sangakupatse nkhondo yoti sungamalize
Chorus