Nyimbo Ikatha
- Genre:Gospel
- Year of Release:2021
Lyrics
Nyimbo Ikatha - Kelvin Sings
...
Kunja kwacha (mavuto ndi omwewa koma tsiku langosintha)
Mdima wagwa(nyimbo ndi yomweyi koma oyimba wango sintha)
Mtima wanga umasweka kale pena ndi yesa ngati ndilibe m'bale
Kusowa oti angandithangate
Tsogolo looneka lopuwala komabe ndiimaba(mwina mavuto nkuzilala)
Misonzi I Kamanga nyumba pamasaya
Confort me zitolilo ndi gitala
Ndikakhala chete makutu mwanga mumaveka nyimbo for some time mtimawu supweteka chowawa chimagwera mkati
Mayeselo a moyo wanga (nyimbo ndi likasa)
Nkhawa ine nkhawa ine (nyimbo ikatha)
see lyrics >>Similar Songs
More from Kelvin Sings
Listen to Kelvin Sings Nyimbo Ikatha MP3 song. Nyimbo Ikatha song from album After The Honesty is released in 2021. The duration of song is 00:03:59. The song is sung by Kelvin Sings.
Related Tags: Nyimbo Ikatha, Nyimbo Ikatha song, Nyimbo Ikatha MP3 song, Nyimbo Ikatha MP3, download Nyimbo Ikatha song, Nyimbo Ikatha song, After The Honesty Nyimbo Ikatha song, Nyimbo Ikatha song by Kelvin Sings, Nyimbo Ikatha song download, download Nyimbo Ikatha MP3 song
Comments (2)
New Comments(2)
Patrick Kawawa
zocci plus
I like you much bro
U give us energy boss oyenda ndo yesu sasowa