
Olakwa Ndani?
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
This song is not currently available in your region.
Lyrics
Olakwa Ndani? - Macelba
...
Olakwa ndani olakwa ndani
pakati pa ochotsa mimba kapena oikana
Okana kholo kapena okana mwana
pakati pa hule loima cha pa stereo
kapena sisitele amene akuyenda ndi ansembeyo
olakwa ndani?
Dona yoti yavutika ndalama ya fees
kuti ayipeze basi agone ndimabiggie
Kapena dolo woti moyo wake sizikuyenda
Kamba koopa moyo wakuba kutenga chingwe nkuzikhweza aah
see lyrics >>Similar Songs
More from Macelba
Listen to Macelba Olakwa Ndani? MP3 song. Olakwa Ndani? song from album After the Silence is released in 2024. The duration of song is 00:02:17. The song is sung by Macelba.
Related Tags: Olakwa Ndani?, Olakwa Ndani? song, Olakwa Ndani? MP3 song, Olakwa Ndani? MP3, download Olakwa Ndani? song, Olakwa Ndani? song, After the Silence Olakwa Ndani? song, Olakwa Ndani? song by Macelba, Olakwa Ndani? song download, download Olakwa Ndani? MP3 song
Comments (2)
New Comments(2)
gertroodes soka
Dunga10
nyimbo iyiyi ikundiwaza
iribhoo