
Corolla ft. Tuno Mw & Hyphen Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Corolla ft. Tuno Mw & Hyphen Mw - Kell Kay
...
u already know ooh
malangizo ndakupasa mtima ndakupasa zonse ndakuuza uuza, usakonde azibambo amabwera ndi zawo penaso matenda aah
Deborah tandivere usafere corolla
Deborah tandivere usafere ndalama
wafera amuna a corolla
wafera amuna a corolla
wafera amuna a corolla
wafera amuna a corolla
zomwe unafesa zija wakolooooora aaaaah wakolora
zomwe unafesa zija wakolooooora aaaah wakolora
HYPHEN
Hey nkhani yanu ili kamwakamwa kufuna kupana wa dollar mpaka kusaka mwana
azako akakuuza kuti sitimakhalana pano dollar yomweyo nosenu mukumagawana zachibwana
umamasuka iwe bola khusa
palibe chinjoyi chimakudusa
owona zithuzi kumati mayi mukupusha
chilichonse mwapanga kwasala kuyamba ubusa
koma amapasa muthawi yake
zipanga zakozo ine singamake
i wish you well zoipa zisakusate
aliyense azaseza mtanda wake
Kelly kay
wafera amuna a corolla
wafera amuna a corolla
wafera amuna a corolla
wafera amuna a corolla
zomwe unafesa zija wakolooooora aaaaah wakolora
zomwe unafesa zija wakolooooora aaaah wakolora
ndinakavera ine
koma chibwana ine
ndinakonda dollar ine
m
m