Holy Water ft. Kineo Madness & Aidfest Madness Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Holy Water ft. Kineo Madness & Aidfest Madness - Kell Kay
...
Yeah
Alright
Y'all ready know
(Kumaloto)
(Siwe wakumaloto mwina)
(Kumaloto)
(Siwe (Tricky Beats ooo) wakumaloto mwina)
Mchere ayy
Usasakanike ndi sugar
Ngati uli pano kufuna kundiyesa
Akupweteketsa wakutuma
Ngati wabwera kuzandiyesa (yesa)
Ngati wabwera kuzandiwerenga (werenga)
Ngati wabwera kuzandiyesa (yesa)
Ngati wabwera kuzandiwerenga (werenga)
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ine zachibwana sikweni kweni
Magwa mu chikondi zeni zeni
Ndipo ukabhowa undimva pain
Nde usandivutitse pusitse
I don't need bad energy in my lifе
Ndimagwira magobo to survive
If you wanna stay show Me love
Ngati uzi gulugusha (Catch a bus)
Mmh tafuma apapa
Funa ndikonzеke tafuma apa
Mmh Ndachi lapa
Zachikondi Zi ndazilapa
Good only vibes wanted out here
Sindikonda za daily
Giving me love and nasilira
Mene mowa Chikondi Mene ndigwilire
Mchere
Usasakanike ndi sugar ooh
Ngati uli pano kufuna kundiyesa
Akupweteketsa wakutuma
Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto)
(Siwe wakumaloto mwina) Ngati wabwera kuzandiwerenga
Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto)
(Siwe wakumaloto mwina) Ngati wabwera kuzandiwerenga
Kumaloto siwe wakumaloto mwina
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ngati ufuna wina
Undiwuze ndikhonzoke eh
Zoti uzindizunza zimenezo zilekeke
Mmh hm
Ma plan ndimasanja ndekha eh
Money ndimasaka ndekha eh
Nde usabwere ndi zondisokoneza eh
Ndikzakuthila Holy water
Mchere
Usasakanike ndi sugar mmh
Ngati uli pano kufuna kundiyesa
Akupweteketsa wakutuma
Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto)
(Siwe wakumaloto mwina) Ngati wabwera kuzandiwerenga
Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto)
(Siwe wakumaloto mwina) ngati wabwera kuzandiwerenga
(Kumaloto siwe wakumaloto mwina) Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ngati wabwera kuzandiyesa
Ngati wabwera kuzandiwerenga
Ngati wabwera kuzandiyesa
Ngati wabwera kuzandiwerenga
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water
Ndikuthila Holy water