
Chonchi ft. Suffix Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Chonchi ft. Suffix Mw - Kell Kay
...
Nthawi Zina, ndimazifusa mukanati simungadye ndikutchila ndiochimwa
ndee bwezi mukudya nokha palibeso nokha
palibeso olo mmodzi otembenuka mtima.
We all, we all fall short olo ntatalikako ndikudziwa
....
Mene ndayendela mbuye bwezi nditafa kale
Ndaswela mitima ine nditalodzedwa kale
Mandisunga bwanji
mandisunga ine
oh no no no