
Mukanabwela ft. Leslie Moyo Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Mukanabwela ft. Leslie Moyo Mw - Kell Kay
...
kell kay ft leslie
tricky beats
you already know
mukanabwera ambuye
mwakhalitsa
nkhani kuno m'dziko lino
n'zodwalitsa
n'zanga analowa mundende
koma ndiosalakwa
family yanga pano zaka
ikungozunzika
tikudikilabe ife
Kodi mubwera liti)x2
ayayayah
yayayah
mukanabwera
ayayayah
yayayah
mwanjimwiza
ana amasiye adzasangalala
Inu mukabwera
ma divorce adzatha onse
Inu mukabwera
ngongolezi zidzayiwalika
Inu mukabwera
matendawa adzatha onse
Inu mukabwera
tikudikilabe ife
Kodi mubwera liti)x2
ayayayah
yayayah
mukanabwera
ayayayah
yayayah
mwanjimwiza)x2
tikondwera mutati
mubwera pompano
azibale aja ambiri
pano tidakayika
imfa yatizunza inu
yatizunza inu mukanabwera
dziko latizunza Inu
latizunza Inu mukanabwera
ayayayah
yayayah
mukanabwera
ayayayah
yayayah
mwanjimwiza)x2