Ndinu ft. Gwamba & Kambwiri Sisters Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Ndinu ft. Gwamba & Kambwiri Sisters - Kell Kay
...
you already Know
ati ndilibe (?) poti ndilibe ndalama
sakumakondwera nane
poti inuyo mwandidalitsa
ati ndine ochimwa!
Ndabeleka ndili mwana, ndine otembeleledwa, banja singalipeze
In every thing I put you first, mumandidalitsabe olo atandipanga curse
adani anga please Jah jah bless(jah jah bless)
chorus
sindimadandaula (oooh) poti zonsee mwapeleka ndinu, ndi malimba mtima (ine) poti zonsee mwapeleka ndinu
simmmalira simmalira ine simmalira ine ( mwapeleka ndinu) usalire usalire iwe usalire
Yoh! thitha kuima pachulu ndi kuchallenger ngati yesu amandikonda angandisale nda? kuyesa kunditchinga
koma madzi alemba nde n