
Ndatopa Lyrics
- Genre:Afropop
- Year of Release:2025
This song is not currently available in your region.
Try the alternative versions below.
Alternative versions:
Lyrics
Ndatopa - Kell Kay
...
(lyrics by Big Bird AKA Siah Nthiwatiwa )
you already know
(exclusive )
just tell me what you want...
iwe tasachedwetsane..
is it the money or fame that you're after..
tandiuze mwina ufuna uphaka lifestyle ..
tamasuka sindufuna ma disaster..
tandiuze nthawi Siri mbali yangaaa
ndiuze ufuna thupi langa..
kapena ndalama zanga..
I am tired every time ndikagwa..
ndimagwa ndekhaaa
ndiuze ufuna thupi langa...
kapena ndalama zanga..
I am tired every time ndikagwa...
ndimagwa ndekhaaa...
ndatopaa nazo..
kutopa ndikusalidwa..
kutopa ndikuzuzidwa..
ndisiye ine....
ndatopaa nazo..
sinakhaleko ndi wangawanga..
anthu amangoswa mtima wanga..
siye ineee
tiye timvaneee..
tiye tisayinirane...
pamapeto tisadzadane..
yeah!
tiye timvane..
bwera tisayinirane..
pamapeto tisadzadane.. yeah!
anthuwa andiononga.. (oonga)
kuononga mbiri yanga (yanganga)
amadintha mawanga..
pano ndisamala ine mtima wanga..
ooh feel iribe hero..
zimayamba bwino uthera mkwiyo..
kumayamba pa high uthera zero..
oh zero
(oh zeroh..)
ndiuze ufuna thupi langa..
kapena ndalama zanga..
iam tired every time ndikagwa..
ndimagwa ndekha..
ndiuze ufuna thupi langa..
kapena ndalamà zanga
iàm tired every time ndikagwa..
ndimagwa ndekhaaa
ndatopaa nazo..
kutopa ndikusalidwa..
kutopa ndikuzuzidwa..
ndisiye inee
ndatopaa nazo..
sinakhalepo ndiwangawanga..
anthu amangoswa mtima wanga..
siye ineee
tiye timvaneee..
bwera tisayinirane..
pamapeto tisadzadane..
yeah!
tiye timvane..
bwera tisayinirane..
pamapeto tisadzadane..
yeah
I've done too much..
I've done too much for love..
I've given my heart too many times..
Kodi chikondicho chidziteroo..
tizidziwiratu mathero..
ngati zimathera uvala velo..
too many times,
ndatopa
ndatopaa nazo..
ndatopa ndikusalidwa..
kutopa ndikuzuzidwa..
ndisiye ine
Ndatopaa nazo..
sinakhaleko ndi wangawanga..
anthu amangoswa mtima wanga..
siye ine
tiye timvaneee..
bwera tisayinirane..
pamapeto tisadzadane..
yeah!
tiye timvaneee..
bwera tisayinirane..
pamapeto tisadzadane..
yeah!
(lyrics by BIG BIRD aka Siah Nthiwatiwa)