![Zanga](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/08/14/f1e8e19599ac46e2ba9c0feb2c3784b5_464_464.jpg)
Zanga Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndipatsireni pen paper ndimulembere mwali
Mwina ndikatenge mic ndiyimbe
Mwina tiyesere ma blocko poti njerwa zimagumuka
Koma bola tichimange chilimbe
Wazipereka nsembe kwakwana
mamuna sayamika uyu nde atipatsire ife tisunge
Ngati watopa nawe
Asiye kukuzunguza, bola ativungire cross tigwire
Poti chikondi sikundende
You supposed to be loved babe
Chikondi kumapeto
Poti chikondi sikundende
You supposed to be loved babe
Chikondi kuma last
Nde udzabwere eh
Bwere eeee zanga
(If you're not happy anymore)
Nde udzabwere eh
Bwere eeee zanga
(If you're not happy anymore)
Come to me babe
Poti Matambala ndi nono
Olo kukhala kungokhalira zisomo mama
Mumtima muli nkhondo
Pali kutsutsana pakati pamikoko eee
Sangasinthe
Sangasiye olo utati bwanji
Wa chake ndi wachake Mamie bola mungosintha plan
Amakuzembera zembera
Khutu unatseka nde zimavuta kunvera
Ukamufunsa amakumemya
Unagwidwa ndi ndende nde ufulu umakuthera
Nobody cares
Nobody cares ungasinthe eee
Nobody cares
Nobody cares ungasinthe eee
Ati chikondi Ndikupilira
Upilira bwanji zopilirazo palibe
Let me take your pain away
Let me your dream guy
Poti chikondi sikundende
You supposed to be loved babe
Chikondi kumapeto
Poti chikondi sikundende
You supposed to be loved babe
Chikondi kuma last
Nde udzabwere eh
Bwere eeee zanga
(If you're not happy anymore)
Nde udzabwere eh
Bwere eeee zanga
(If you're not happy anymore)
Come to me babe