PANO Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
PANO - Driemo Mw
...
is this a joke? are you kidding me ukutanthauza chani zachuluka ndi nkhani planning to leave me I'm I afool for falling for you? tadutsa muzambili tapangadi zambili and now you want to switch like that? oooh Kodi ndaipa pano? ndakubhowa pano zonse zija wandichititsa zikaipe pano? Kodi ndaipa pano ndakubhowa pano zonse zija wandiphunzitsa zikaipe lelo? unandiyambitsa shisha,mowa Mesa ndi iwe iwe na ine ku ma club everyday lelo ukuti Khalidwe la banja mwaine mulibe Kodi ndi game ya mtundu wanji you're playing nde unkandisinthilanji nde unkandisinthilanji ooh my guy fees yako itashupa ndinagulitsa Munda ine lelo unagwidwa ndi shasha wati ine wakumunda koma izizi ndimkapanga chifukwa ndimasamala zaife ineyo ndinkablanda kufuna kukusangalatsa iwe how I wish I could go back