Mapiko Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Mapiko - Driemo Mw
...
boy from kekelo mmmmm ye ine ukati unisamale nao anzanga onse ubasaraze ine Zimbabwe iwe ukhale malao umaziba monitakwanya maso atooona mutima unasunga mutuwanga wasimikiza namupeza onisamala ndiwe cimwemwe changa (umabwela cakumamawa) bwenzi lamoyo wanga and then I say ngati siyiweeeyoo ine kulibeso wina ngati siyineeeyooo sungasankheso wina coz the way that I love u (the way that I love u) the way that u love me(the way that u love me) love the way that u treeeat me,,ndiwe ngelo wopanda mapiko,, zonse umo umo,, love u so more,,,,loving u by my side ndicisomo,,ndirindiwoyenda naaaaye ( ndimangokamba)ndiri ndiocheza naaaye (sindidela nkhawa)komwe nding- aKale konko wathamangisa magazine yamphongo baby wanitesa nkhongono sindingapitile tela mpompo,,,ine yeeeee,(angati siyiiiweyo ine kulibenso wina )(ngati siyiiineeyo sungasankheso wina),,,coz the way that I love u (the way that I love u). the way that u love me (the way that u love me) love the way that u treat me ,,,,ndiwe ngelo wopanda mapiko,,,,,mapiko mapiko loving the way that u call me stazi,, Darling,, Babe,,Boo love me the way that and yo body ine,,,ngati siyiiiweyo kulibeso wina,,,ngati siyiiineeyo sungasankheso wina