Weni Weni Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Weni Weni - Driemo Mw
...
Yeah
Its driemo
Ukali mbulu munthiti mose ngati mwaomba bulu
Ndimakunyoza ndigulu
Alira bwanji munthu wankulukulu oooh
Eya unkadalira you never know she could
leave like that
Eya unkakaika you never know he could leave like that
Koma mtima ukati sweeke(sweke)
Umayang’ana pali dzenje (dzenje)
Kuti bora mwina ndizagwere (gwere)
Ndizabvomereza indimeze nthakayi
Sanakulande pachiyambi she didn’t ’ belong to you
Sanakulande pachiyambi he didn’t belong to you
Poti mwamuna weniweni salandika, sathawa
Poti nkazi weniweni salandika, sathawa owwwh oooh
eya ndokongola, ululu umakukomola usiku sugona
Umangokhalira ku moana aaaah
Inde sankakukonda no matter how many times she said
Eya sankakufuna no matter how many times he showed it
Stop fighting for the losing battle
Yang’ana za tsogolo lako naweso you deserve chikondi
Naweso you deserve to be happy
Sanakulande pachiyambi she didn’t ’ belong to you
Kaya sanakulande pachiyambi he didn’t ’ belong to you
Poti mwamuna weniweni salandika, sathawa
Poti nkazi weniweni salandika, sathawa owwwh oooh
Ngati chili chako ooh chako
Ngati chili changa oooh changa
Palibe angachilande palibe angachitenge
palibe angakulonde palibe angakutengere
Sanakulande pachiyambi she didn’t
Eya sanakulande pachiyambi he didn’t ’ belong to you