Compensation Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Compensation - Driemo Mw
...
driemo.......
oh mtima upereke
kwa ine ndiutenge
don't worry about safety
ndidzachengetera chengereta
I know mtima unaswekapo
you have been there unalirapo
ululu mu mtima kufikapo
ukaganidzira ganizira ganizira
pa iwe ndilora ndipepera
chikondi chisaperewere
or pa ground paterere
I will love you the same beib....
oh udzandifunse..
mkadzakuswera mtima udzandifunse
kuti mwina compensation....
ndidzapereke moyo wangawu ×2
Don't be sacred to love me more
zakale zapita it's me and you
undiudze pomwe Pali mantha ako
I know mtima umakana ukandiunika
umaona ngat aja anakunamidza
koma I wanna be your soudjer, your fighter, protecter ,defender, I just wanna be your friend for love....
oh udzandifunse..
mkadzakuswera mtima udzandifunse
kuti mwina compensation....
ndidzapereke moyo wangawu ×2