Duma Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Duma - Driemo Mw
...
In a blink of an eye
wasomphola mtima niubongo
mtendere wanga ngati sine mwini khomo
ine koma tetelite
mtima ngati ndimatenda
zoona alidedelide
limodzi mpaka titayenda
zonse unatenga the moment I saw you
Mtima unapempha momvetsa chisoni
zonse unatenga the moment I saw you
Mtima unapempha pempha ngakhale waaaa
mtima wanga umadumpha when I see your face
ndimakhala ndi phuma whenever your body next to me
and it goes like
duma
duma
duma
duma
duma
and it sings like
duma
duma
duma
duma
duma
and the song goes
duma
duma
duma
duma
duma
and it goes like
duma
duma
duma
duma
duma