Intro (Pray For Me) Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Uh yeah yeah
Mama pick up the phone
I really need someone to talk to
Mama pick the phone yeah
Cause your son is in battles
I don't really know if I can win this
All I need is your wisdom uh yeah
Dziko ladzadza ndima bonzo
Kukhalira chitonzo
I don't really know kani zimakhala choncho
Ndifuna mundigwire nkono
Oooh!
Mama pray for me
Pray for memudzindipempherera!
Mama pray for me
Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me
Pray for memudzindipempherera!
Mama pray for me
Pray for me konse ndingayende ine eee
Mama answer my questions
Cause I don't know the reasons
Why people are faking love
Faking happy life
Kubisala muzithunzi zosekerera
Kuseli akunjenjemera
Nobody Nobody seems real
Aliyense ali choncho
(Nde)
Zikadzandivuta mayiwanga
Mudzandiitane mwana wanga bwera bwera
Bwera
There is light
At the end of this tunnel
Mama pray for me
Pray for memudzindipempherera!
Mama pray for me
Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me
Pray for memudzindipempherera!
Mama pray for me
Pray for me konse ndingayende ine eee
Mayi mukapinda bondo
Mukapinda bondo
Mamie mukapinda bondo
Mukapinda bondo
Mapemphero amayankhidwa
Zitseko zimatsekuka
Mayi mukapinda bondo
So pray for me!
Pray for me!
Mama pray for me
Pray for memudzindipempherera!
Mama pray for me
Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me
Pray for memudzindipempherera!
Mama pray for me
Pray for me konse ndingayende ine eee