
Chilembwe Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Chilembwe - Eli Njuchi
...
john chilembwe aah (njuchi)
sitinavane mphete
abale munthune ndimveni
sindikonda ndalama chete
nkhani ndimaresponsebility(iwee)
moyo so movie
one time sumalipira bill
kukongola sikumagula ufa
mwana wa eni ukamdyetsa Chan
(chorus)
banja musalipute bambo mulibe chilembwe
chifukwa sichina bambo nthumba mulibe chilembwe
mbumba tisadziyambe kasakeni chilembwe
nalo banja limafunika john (eh) chilembwe
chilembwe(chilembwe)john chilembwe
oh chilembwe(chilembwe)john chilembwe