Dzina Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Dzina - Eli Njuchi
...
Dzina
ndi dzina liti lingadzakhale
mwina ndi ma twins wina wamuna wina wamkaz
Julie
I have wrote a letter for you
mwina John have wrote a letter for you
lero my future daughter how is school
ngati umakonda adad give me hie 5
lero my future son Geri ili bwanj
ngat ndili pafupi ubwere undihage
pakanali pano sindinakumane ndi amayi.ako
one thing I Know she is a loving and caring lady
za obvios iam funniest father
za obvious iam am very this father
ukamandiona mu future
dziwa ndine hero ngati ukumadya kugona
sound it great ful
2020 tu mwanawe it's a tough time for ur father
ma pressure ma pressure mwana wamamuna ma pressure
ndikanali vendor
searching for ur better life for me baba
kwa ulova
fighting for your better future ku Limbe
ngati ndiike
chank fast forward
Pena ngati ndi ngogiver ndikut fast forward
what is it comes,,,,, is it goes my daughter
patience
ndili kubwera seen
soon my son confidence
Dzinaaaa ndi dzina liti lingadzakhale
(suspense)
Dzina ndi dzina lit lingadzakhale