Someti Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Oh no
Njuchi
J mus iwe
Oky oky
One time one time
Reload
Oky x2
(Hook)
Ukampeza soulmate waine
Umuuze ndamusowa
Ukampeza soulmate waine
Umuuze ndamusowa
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ndamusowa
(Ndamusowa eeh)
(Nyimbo zapa Dowa boma
coming up right away)
Ndatopa zongokhalira kulota
Abwela liti mu moyo mwane
Ndatopa zongokhalira kulira
Abwela liti mu moyo mwane
Onse si different story
Ena osewa zimathela kumvela Maury nde
Mundimveleko chisoni
Ndikufund soulmate
Ukampeza soulmate waine
Umuuze ndamusowa
Ukampeza soulmate waine
Umuuze ndamusowa
Ndamusowa
Ndamusowa)
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ndamusowa
(My soulmate ndakusowa)
Ndati mvelako kanyimbo
(Soulmate)
Tabwela iwe
(My soulmate ndakusowa)
Mpaka ndalemba nyimbo
(Soulmate)
Are you there
(My soulmate ndakusowa)
Ukuchedwa ukuchedwa
(Soulmate)
(Nyimbo zapa dowa boma)
(My soulmate ndakusowa)
Tidza mange nyumba
For you and me tiza Dzadzemo mbumba
Tidza sake chuma
For you and me tisa dzasowe nsima
Too many plans that i have for you
Love of my life tell me where are you
From my heart i am missing you
Undimvele soulmate iwe
Mwina ndi mzungu
Mwina ngwaku Gelemani
Mwina ndi Chinese!
Mwina samamva kanthu
Mwina anabadwa wakhungu
Tidzapeza means Ngati ali patali ech
Uthenga umupeze Konko ku Halale
sadlim&8d9kg chisoni Netikufuna
Ukampeza soulmate waine
Umuuze ndamusowa
Ukampeza soulmate waine
Umuuze ndamusowa
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ndamusowa
(Ndamusowa)
Ooh yeah yeah
{Fumbimbi}
(Soulmate)
Tabwela iwe
(My soulmate ndakusowa)
Ndati mvelako kanyimbo
(Soulmate)
Tabwela iwe
(My soulmate ndakusowa)
Mpaka ndalemba nyimbo
(Soulmate)
Are you there
(My soulmate ndakusowa)
Ukuchedwa ukuchedwa
(Soulmate)
(My soulmate ndakusowa)